Yesaya 51:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti njenjete idzawadya ngati copfunda, ndi mbozi zidzawadya ngati ubweya; koma cilungamo canga cidzakhala ku nthawi zonse, ndi cipulumutso canga ku mibadwo yonse.

Yesaya 51

Yesaya 51:4-12