Yesaya 5:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsoka kwa iwo amene aphatikiza nyumba ndi nyumba, amene alumikiza munda ndi munda, kufikira padzapanda malo, ndipo inu mudzasiyidwa nokha pakati pa dziko!

Yesaya 5

Yesaya 5:4-18