Yesaya 5:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

palibe amene adzalema, kapena adzapunthwa mwa iwo, palibe amene adzaodzera kapena kugona tulo; ngakhale lamba la m'cuuno mwao silidzamasuka, kapena comangira ca nsapato zao sicidzaduka;

Yesaya 5

Yesaya 5:25-30