Yesaya 5:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Iye adzakwezera a mitundu yakutari mbendera, nadzawayimbira mluzu, acokere ku malekezero a dziko; ndipo taonani, iwo adzadza ndi liwiro msanga msanga;

Yesaya 5

Yesaya 5:24-28