Yesaya 48:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

cifukwa cace ndinakudziwitsa ici kuyambira kale; cisanaoneke ndinakusonyeza ico, kuti iwe unganene, Fano langa lacita izo, ndi cifanizito canga cosema, ndi cifaniziro canga coyenga zinazilamulira.

Yesaya 48

Yesaya 48:1-11