Yesaya 46:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kumbukirani zinthu zoyamba zakale, kuti Ine ndine Mulungu, ndipo palibenso wina; Ine ndine Yehova, ndipo palibenso wina wofana ndi Ine;

Yesaya 46

Yesaya 46:1-13