Yesaya 46:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndilalikira za cimariziro kuyambira paciyambi, ndi kuyambira nthawi zakale ndinena zinthu zimene zisanacitidwe; ndi kunena, Uphungu wanga udzakhala, ndipo ndidzacita zofuna zanga zonse;

Yesaya 46

Yesaya 46:1-13