Yesaya 45:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Sonkhanani nokha, mudze; yandikirani cifupi pamodzi, inu amene mwapulumuka amitundu; iwo alibe nzeru, amene anyamula mtengo wa fano lao losema, ndi kupemphera mlungu wosakhoza kupulumutsa.

Yesaya 45

Yesaya 45:18-24