Yesaya 43:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ine, Inedi, ndine amene ndifafaniza zolakwa zako, cifukwa ca Ine mwini; ndipo Ine sindidzakumbukira macimo ako.

Yesaya 43

Yesaya 43:15-28