Yesaya 42:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taona, zinthu zakale zaoneka, ndipo zatsopano Ine ndizichula; zisanabuke ndidzakumvetsani.

Yesaya 42

Yesaya 42:4-14