Yesaya 42:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ine ndine Yehova; dzina langa ndi lomweli; ndipo ulemerero wanga Ine sindidzapereka kwa wina, ngakhale kunditamanda kwa mafano osemedwa.

Yesaya 42

Yesaya 42:4-15