Yesaya 37:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taonani, ndidzaika mzimu mwa iye, ndipo iye adzamva mbiri, nadzabwerera kunka ku dziko la kwao; ndipo ndidzamgwetsa ndi lupanga m'dziko la kwao.

Yesaya 37

Yesaya 37:3-14