Yesaya 37:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yesaya anati kwa iwo, Mukati kwa mbuyanu, Atero Yehova, musaope mau amene wawamva iwe, amene atumiki a mfumu ya Asuri andilalatira Ine.

Yesaya 37

Yesaya 37:1-7