Yesaya 37:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti mudzaoneka m'Yerusalemu, otsala ndi opulumuka m'Yerusalemu, otsala ndi opulumuka m'phiri la Ziyoni; cangu ca Yehova wa makamu cidzacita ici.

Yesaya 37

Yesaya 37:26-38