Yesaya 37:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anaponya milungu yao pamoto; pakuti iyo sinali milungu, koma nchito yopangidwa ndi manja a anthu, mtengo ndi mwala; cifukwa cace iwo anaiononga,

Yesaya 37

Yesaya 37:10-23