Yesaya 31:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mwala wace udzacoka, cifukwa ca mantha, ndi akalonga ace adzaopa mbendera, ati Yehova, amene moto wace uli m'Ziyoni, ndi ng'anjo yace m'Yerusalemu.

Yesaya 31

Yesaya 31:1-9