Yesaya 31:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Asuri adzagwa ndi lupanga losati la munthu; ndi lupanga losati la anthu lidzammariza iye; ndipo iye adzathawa lupanga, ndi anyamata ace adzalamba.

Yesaya 31

Yesaya 31:1-9