Yesaya 30:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo nthawi zonse Yehova adze vakantha ndi ndodo yosankhikayo, padzamveka mangaka ndi zeze; ndi m'nkhondo zothunyana-thunyana, Iye adzamenyana nao.

Yesaya 30

Yesaya 30:28-33