Yesaya 29:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova wa makamu adzamzonda ndi bingu, ndi cibvomezi, ndi mkokomo waukuru, kabvumvulu, ndi mkuntho, ndi lawi la moto wonyambita.

Yesaya 29

Yesaya 29:1-14