Yesaya 29:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma khamu la acilendo ako lidzafanana ndi pfumbi losalala, ndi khamu la oopsya lidzakhala monga mungu wocokacoka; inde kudzaoneka modzidzimuka dzidzidzi.

Yesaya 29

Yesaya 29:1-8