Yesaya 29:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo buku laperekedwa kwa wosadziwa kuwerenga, ndi kuti, Werengani umu; koma ati, Ine sindinaphunzira.

Yesaya 29

Yesaya 29:8-15