Yesaya 28:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma iwonso adzandima ndi vinyo, nasocera ndi cakumwa caukali, wansembe ndi mneneri adzandima ndi cakumwa caukali, iwo amezedwa ndi vinyo, nasocera ndi cakumwa caukali, adzandima popenya, napunthwa poweruza.

Yesaya 28

Yesaya 28:3-17