Yesaya 28:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo adzakhala mzimu wa ciweruziro kwa oweruza mirandu, ndi mphamvu kwa iwo amene abweza nkhondo pacipata.

Yesaya 28

Yesaya 28:3-8