Yesaya 28:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nthawi zonse umapita, udzakutengani; cifukwa m'mawa ndi m'mawa udzapita, usana ndi usiku; ndipo kudzakhala kuopsya kokha, kumva mbiri yace.

Yesaya 28

Yesaya 28:16-23