Yesaya 26:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Inde m'njira ya maweruziro anu, Yehova, ife talindira Inu; moyo wathu ukhumba dzina lanu, ndi cikumbukilo canu.

Yesaya 26

Yesaya 26:4-13