Yesaya 26:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ife tinali ndi pakati, ife tinamva zopweteka, tafanana ngati tabala mphepo; sitinacite cipulumutso ciri conse pa dziko lapansi; ngakhale okhala m'dziko lapansi sanagwe.

Yesaya 26

Yesaya 26:17-21