Yesaya 17:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa iwe waiwala Mulungu wa cipulumutso cako, sunakumbukira thanthwe la mphamvu zako; cifukwa cace iwe waoka mitengo yokondweretsa, waokapo zipinjiri zacilendo;

Yesaya 17

Yesaya 17:2-14