Yesaya 13:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Babulo, ulemerero wa maufumu, mudzi wokongolawo Akasidi anaunyadira, adzakhala monga momwe Mulungu anapasula Sodomu ndi Gomora.

Yesaya 13

Yesaya 13:12-22