Yesaya 13:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzalanga dziko lapansi, cifukwa ca kuipa kwao, ndi oipa cifukwa ca mphulupulu zao; ndipo ndidzaletsa kudzikuza kwa onyada, ndidzagwetsa kudzikweza kwa oopsya.

Yesaya 13

Yesaya 13:7-19