Yesaya 13:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa nyenyezi za kumwamba ndi makamu ao sizidzawala; dzuwa lidzada m'kuturuka kwace, ndipo mwezi sudzaonetsa kuwala kwace.

Yesaya 13

Yesaya 13:6-15