Yeremiya 6:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yehova wa makamu atero, Adzakunkha otsalira a Israyeli monga mpesa; bweza dzanja lako monga wakuchera mphesa m'mitanga yace.

Yeremiya 6

Yeremiya 6:2-17