Yeremiya 6:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndidzanena ndi yani, ndidzacita mboni kwa yani, kuti amve? Taona khutu lao liri losadulidwa, ndipo sangathe kumva; taona, mau a Yehova awatonzetsa iwo; sakondwera nao.

Yeremiya 6

Yeremiya 6:4-11