Yeremiya 52:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo korona wamkuwa anali pamwamba pace; utari wace wa korona mmodzi unali wa mikono isanu, ndi made ndi makangaza pakorona pozungulira pace, onse amkuwa: nsanamira inzace yomwe inali nazo zonga zomwezi, ndi makangaza.

Yeremiya 52

Yeremiya 52:12-27