Yeremiya 52:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma nsanamirazo, utari wace wa nsanamira yina unafikira mikono khumi mphambu isanu ndi itatu; ndi cingwe ca mikono khumi ndi iwiri cinaizinga; kucindikira kwace kunali zala zinai; inali yagweregwere.

Yeremiya 52

Yeremiya 52:15-22