Yeremiya 51:35 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Wokhala m'Ziyoni adzati, Ciwawa anandicitira ine ndi thupi langa cikhale pa Babulo; nadzati Yerusalemu, Mwazi wanga ukhale pa okhala m'Kasidi.

Yeremiya 51

Yeremiya 51:25-39