Yeremiya 48:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Za Moabu Atero Yehova wa makamu, Mulungu wa Israyeli: Tsoka Nebo! pakuti wapasuka; Kiriyataimu wacitidwa manyazi, wagwidwa; linga la pamtunda lacitidwa manyazi lapasudwa.

Yeremiya 48

Yeremiya 48:1-9