Yeremiya 44:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace atero Yehova wa makamu, Mulungu wa Israyeli: Taonani, ndidzayang'anitsa nkhope yanga pa inu ndikucitireni inu coipa, ndidule Yuda lonse.

Yeremiya 44

Yeremiya 44:3-18