Yeremiya 44:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Sanadzicepetse mpaka lero lomwe, sanaope, sanayende m'cilamulo canga, kapena m'malemba anga, amene ndinaika pamaso panu ndi pa makolo anu.

Yeremiya 44

Yeremiya 44:5-19