Yeremiya 43:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Yohanani mwana wace wa Kareya, ndi akazembe onse: a nkhondo, anatenga otsala onse a Yuda, amene anabwera ku mitundu yonse kumene anaingitsidwirako kuti akhale m'dziko la Yuda;

Yeremiya 43

Yeremiya 43:4-12