Yeremiya 43:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yohanani mwana wace wa Kareya, ndi akazembe onse a nkhondo, ndi anthu onse sanamvera mau a Yehova, kuti akhale m'dziko la Yuda.

Yeremiya 43

Yeremiya 43:1-13