Yeremiya 41:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma mwa iwo anaoneka anthu khumi amene anati kwa Ismayeli, Musatiphe ife; pakuti tiri ndi cuma cobisika m'mudzi, ca tirigu, ndi ca barele, ndi ca mafuta, ndi ca uci. Momwemo analeka, osawapha pakati pa abale ao.

Yeremiya 41

Yeremiya 41:1-10