Yeremiya 41:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo panali, pamene analowa pakati pa mudzi, Ismayeli mwana, wa Netaniya anawapha, nawaponya pakati pa dzenje, iye ndi anthu okhala naye.

Yeremiya 41

Yeremiya 41:2-17