Yeremiya 39:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo panali pamene Zedekiya mfumu ya Yuda ndi amuna onse a nkhondo anawaona, anathawa naturuka m'mudzi usiku, panjira pa munda wa mfumu, pa cipata ca pakati pa makoma awiri; ndipo iye anaturukira pa njira ya kucidikha.

Yeremiya 39

Yeremiya 39:2-6