Yeremiya 39:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo akuru onse a mfumu ya ku Babulo analowa, nakhala m'cipata capakati, Nerigalisarezara, Samgari Nebo, Sarisekimu, mkuru wa adindo, Nerigalisarezara mkuru wa alauli ndi akuru ena onse a mfumu ya ku Babulo.

Yeremiya 39

Yeremiya 39:1-7