Yeremiya 39:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ndidzakupulumutsatu ndipo sudzagwa ndi lupanga, koma udzakhala nao moyo wako ngati cofunkha, pakuti wandikhulupirira Ine, ati Yehova.

Yeremiya 39

Yeremiya 39:11-18