Yeremiya 39:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ndidzakupulumutsa tsiku lomwelo, ati Yehova: ndipo sudzaperekedwa m'manja a anthu amene uwaopa.

Yeremiya 39

Yeremiya 39:13-18