Yeremiya 38:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yehova atero, Iye wakukhala m'mudziwu adzafa ndi lupanga, ndi njala, ndi caola; koma iye wakuturukira kunka kwa Akasidi adzakhala ndi moyo, ndipo adzakhala nao moyo wace ngati cofunkha, nadzakhala ndi moyo.

Yeremiya 38

Yeremiya 38:1-10