Yeremiya 38:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Sefatiya mwana wa Matani ndi Gedaliya mwana wa Pusuri, ndi Yukali mwana wa Selemiya, ndi Pasuri mwana wa Malikiya, anamva mau amene Yeremiya ananena ndi anthu onse, kuti,

Yeremiya 38

Yeremiya 38:1-2