Yeremiya 34:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Zedekiya mfumu ya Yuda ndi akulu ace ndidzawapereka m'dzanja la adani ao, ndi m'dzanja la akufuna moyo wao, ndi m'dzanja la nkhondo ya mfumu ya ku Babulo, imene yakucokerani.

Yeremiya 34

Yeremiya 34:16-22