Yeremiya 34:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndidzapereka iwo m'dzanja la adani ao, ndi m'dzanja la iwo akufuna moyo wao; ndipo mitembo yao idzakhala cakudya ca mbalame za mlengalenga, ndi ca zirombo za pa dziko lapansi.

Yeremiya 34

Yeremiya 34:13-22